Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yakobo 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho gonjerani Mulungu,+ koma tsutsani Mdyerekezi+ ndipo adzakuthawani.+

  • 1 Yohane 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Tikudziwa kuti ndife anthu a Mulungu, koma dziko lonse lili mʼmanja mwa woipayo.*+

  • Chivumbulutso 12:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndinamva mawu ofuula kumwamba akuti:

      “Tsopano chipulumutso,+ mphamvu, Ufumu wa Mulungu wathu+ ndi ulamuliro wa Khristu wake zafika, chifukwa woneneza abale athu waponyedwa pansi. Iye amawaneneza masana ndi usiku pamaso pa Mulungu wathu.+ 11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa+ ndiponso chifukwa cha uthenga umene ankalalikira+ ndipo anali okonzeka kufa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena