6 Patsogolo pa mpando wachifumuwo, panali chinachake chooneka ngati nyanja ya galasi+ komanso ngati mwala wa kulusitalo.
Pakati pa mpando wachifumuwo ndiponso kuzungulira mpandowo, panali angelo 4+ amene anali ndi maso ambirimbiri, kutsogolo ndi kumbuyo komwe.