Luka 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndikukuuzani kuti, aliyense amene akuvomereza pamaso pa anthu kuti ndi wophunzira wanga,+ Mwana wa munthunso adzamuvomereza pamaso pa angelo a Mulungu kuti ndi wophunzira wake.+ 1 Yohane 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Aliyense amene amakana Mwana sangakhale pa ubwenzi ndi Atate.+ Koma amene amavomereza Mwana+ amakhalanso pa ubwenzi ndi Atate.+
8 Ndikukuuzani kuti, aliyense amene akuvomereza pamaso pa anthu kuti ndi wophunzira wanga,+ Mwana wa munthunso adzamuvomereza pamaso pa angelo a Mulungu kuti ndi wophunzira wake.+
23 Aliyense amene amakana Mwana sangakhale pa ubwenzi ndi Atate.+ Koma amene amavomereza Mwana+ amakhalanso pa ubwenzi ndi Atate.+