Numeri 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pajatu akazi amenewa ndi amene anatsatira mawu a Balamu nʼkunyengerera Aisiraeli kuti achimwire Yehova+ pa zimene zinachitika ku Peori,+ moti mliri unagwera gulu la anthu a Yehova.+ 2 Petulo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Asocheretsedwa chifukwa anasiya njira yowongoka. Atsatira njira ya Balamu+ mwana wa Beori, amene anachita zinthu zoipa chifukwa chofunitsitsa kulandira mphoto,+ Yuda 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ali ndi tsoka chifukwa atsatira njira ya Kaini,+ asankha njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto ndipo awonongeka polankhula moukira+ ngati Kora.+
16 Pajatu akazi amenewa ndi amene anatsatira mawu a Balamu nʼkunyengerera Aisiraeli kuti achimwire Yehova+ pa zimene zinachitika ku Peori,+ moti mliri unagwera gulu la anthu a Yehova.+
15 Asocheretsedwa chifukwa anasiya njira yowongoka. Atsatira njira ya Balamu+ mwana wa Beori, amene anachita zinthu zoipa chifukwa chofunitsitsa kulandira mphoto,+
11 Ali ndi tsoka chifukwa atsatira njira ya Kaini,+ asankha njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto ndipo awonongeka polankhula moukira+ ngati Kora.+