Mabuku a M’baibulo ndi Tsatanetsatane Wake
Mabuku a Malemba Achiheberi Nthawi Yachikhristu Isanafike
Dzina la Buku: Genesis
Wolemba: Mose
Kumene Analembera: M’chipululu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): 1513
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): “Pa chiyambi” mpaka 1657
Dzina la Buku: Ekisodo
Wolemba: Mose
Kumene Analembera: M’chipululu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): 1512
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): 1657-1512
Dzina la Buku: Levitiko
Wolemba: Mose
Kumene Analembera: M’chipululu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): 1512
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): Mwezi umodzi (1512)
Dzina la Buku: Numeri
Wolemba: Mose
Kumene Analembera: M’chipululu ndi M’chigwa cha Mowabu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): 1473
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): 1512-1473
Dzina la Buku: Deuteronomo
Wolemba: Mose
Kumene Analembera: M’chigwa cha Mowabu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): 1473
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): Miyezi iwiri (1473)
Dzina la Buku: Yoswa
Wolemba: Yoswa
Kumene Analembera: Kanani
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 1450
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): 1473–c. 1450
Dzina la Buku: Oweruza
Wolemba: Samueli
Kumene Analembera: Isiraeli
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 1100
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): c. 1450–c. 1120
Dzina la Buku: Rute
Wolemba: Samueli
Kumene Analembera: Isiraeli
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 1090
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): Zaka 11 za ulamuliro wa Oweruza
Dzina la Buku: 1 Samueli
Wolemba: Samueli, Gadi, Natani
Kumene Analembera: Isiraeli
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 1078
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): c. 1180-1078
Dzina la Buku: 2 Samueli
Wolemba: Gadi, Natani
Kumene Analembera: Isiraeli
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 1040
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): 1077–c. 1040
Dzina la Buku: 1 Mafumu
2 Mafumu
Wolemba: Yeremiya
Kumene Analembera: Yuda ndi Iguputo
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): Mpukutu umodzi, 580
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): c. 1040-580
Dzina la Buku: 1 Mbiri
2 Mbiri
Wolemba: Ezara
Kumene Analembera: Yerusalemu (?)
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): Mpukutu umodzi, c. 460
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): Kuchokera pa 1 Mbiri 9:44: 1077-537
Dzina la Buku: Ezara
Wolemba: Ezara
Kumene Analembera: Yerusalemu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 460
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): 537–c. 467
Dzina la Buku: Nehemiya
Wolemba: Nehemiya
Kumene Analembera: Yerusalemu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): a. 443
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): 456–a. 443
Dzina la Buku: Esitere
Wolemba: Moredekai
Kumene Analembera: Susani, Elamu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 475
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): 493–c. 475
Dzina la Buku: Yobu
Wolemba: Mose
Kumene Analembera: M’chipululu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 1473
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): Kuposa zaka 140 pakati pa 1657 ndi 1473
Dzina la Buku: Masalimo
Wolemba: Davide ndi ena
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 460
Dzina la Buku: Miyambo
Wolemba: Solomo; Aguri; Lemueli
Kumene Analembera: Yerusalemu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 717
Dzina la Buku: Mlaliki
Wolemba: Solomo
Kumene Analembera: Yerusalemu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): b. 1000
Dzina la Buku: Nyimbo ya Solomo
Wolemba: Solomo
Kumene Analembera: Yerusalemu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 1020
Dzina la Buku: Yesaya
Wolemba: Yesaya
Kumene Analembera: Yerusalemu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): a. 732
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): c. 778–a. 732
Dzina la Buku: Yeremiya
Wolemba: Yeremiya
Kumene Analembera: Yuda; Iguputo
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): 580
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): 647-580
Dzina la Buku: Maliro
Wolemba: Yeremiya
Kumene Analembera: Pafupi ndi Yerusalemu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): 607
Dzina la Buku: Ezekieli
Wolemba: Ezekieli
Kumene Analembera: Babulo
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 591
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): 613–c. 591
Dzina la Buku: Danieli
Wolemba: Danieli
Kumene Analembera: Babulo
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 536
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): 618–c. 536
Dzina la Buku: Hoseya
Wolemba: Hoseya
Kumene Analembera: Samariya (Chigawo)
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): a. 745
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): b. 804–a. 745
Dzina la Buku: Yoweli
Wolemba: Yoweli
Kumene Analembera: Yuda
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 820 (?)
Dzina la Buku: Amosi
Wolemba: Amosi
Kumene Analembera: Yuda
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 804
Dzina la Buku: Obadiya
Wolemba: Obadiya
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 607
Dzina la Buku: Yona
Wolemba: Yona
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 844
Dzina la Buku: Mika
Wolemba: Mika
Kumene Analembera: Yuda
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): b. 717
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): c. 777-717
Dzina la Buku: Nahumu
Wolemba: Nahumu
Kumene Analembera: Yuda
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): b. 632
Dzina la Buku: Habakuku
Wolemba: Habakuku
Kumene Analembera: Yuda
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): c. 628 (?)
Dzina la Buku: Zefaniya
Wolemba: Zefaniya
Kumene Analembera: Yuda
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): b. 648
Dzina la Buku: Hagai
Wolemba: Hagai
Kumene Analembera: Yerusalemu Womangidwanso
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): 520
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): Masiku 112 (520)
Dzina la Buku: Zekariya
Wolemba: Zekariya
Kumene Analembera: Yerusalemu Womangidwanso
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): 518
Nthawi ya Zochitikazo (B.C.E.): 520-518
Dzina la Buku: Malaki
Wolemba: Malaki
Kumene Analembera: Yerusalemu Womangidwanso
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (B.C.E.): a. 443
Mabuku a Malemba Achigiriki Olembedwa M’nthawi Yachikhristu
Dzina la Buku: Mateyu
Wolemba: Mateyu
Kumene Analembera: Palesitina
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 41
Nthawi ya Zochitikazo: 2 B.C.E.–33 C.E.
Dzina la Buku: Maliko
Wolemba: Maliko
Kumene Analembera: Roma
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 60-65
Nthawi ya Zochitikazo: 29-33 C.E.
Dzina la Buku: Luka
Wolemba: Luka
Kumene Analembera: Kaisareya
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 56-58
Nthawi ya Zochitikazo: 3 B.C.E.–33 C.E.
Dzina la Buku: Yohane
Wolemba: Mtumwi Yohane
Kumene Analembera: Efeso, kapena chapafupi
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 98
Nthawi ya Zochitikazo: Pambuyo pa mawu oyamba, 29-33 C.E.
Dzina la Buku: Machitidwe
Wolemba: Luka
Kumene Analembera: Roma
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 61
Nthawi ya Zochitikazo: 33–c. 61 C.E.
Dzina la Buku: Aroma
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Korinto
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 56
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: 1 Akorinto
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Efeso
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 55
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: 2 Akorinto
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Makedoniya
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 55
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: Agalatiya
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Korinto kapena Antiokeya wa ku Siriya
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 50-52
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: Aefeso
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Roma
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 60-61
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: Afilipi
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Roma
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 60-61
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: Akolose
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Roma
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 60-61
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: 1 Atesalonika
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Korinto
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 50
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: 2 Atesalonika
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Korinto
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 51
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: 1 Timoteyo
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Makedoniya
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 61-64
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: 2 Timoteyo
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Roma
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 65
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: Tito
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Makedoniya (?)
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 61-64
Dzina la Buku: Filimoni
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Roma
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 60-61
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: Aheberi
Wolemba: Paulo
Kumene Analembera: Roma
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 61
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: Yakobo
Wolemba: Yakobo (m’bale wa Yesu)
Kumene Analembera: Yerusalemu
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): b. 62
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: 1 Petulo
Wolemba: Petulo
Kumene Analembera: Babulo
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 62-64
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: 2 Petulo
Wolemba: Petulo
Kumene Analembera: Babulo (?)
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 64
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: 1 Yohane
Wolemba: Mtumwi Yohane
Kumene Analembera: Efeso, kapena chapafupi
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 98
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: 2 Yohane
Wolemba: Mtumwi Yohane
Kumene Analembera: Efeso, kapena chapafupi
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 98
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: 3 Yohane
Wolemba: Mtumwi Yohane
Kumene Analembera: Efeso, kapena chapafupi
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 98
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: Yuda
Wolemba: Yuda (m’bale wa Yesu)
Kumene Analembera: Palesitina (?)
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 65
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku: Chivumbulutso
Wolemba: Mtumwi Yohane
Kumene Analembera: Patimo
Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.): c. 96
Nthawi ya Zochitikazo:
Dzina la Buku Wolemba Kumene Analembera Nthawi Imene Anamaliza Kulemba (C.E.) Nthawi ya Zochitikazo
[Mayina a anthu amene analemba mabuku ena ndi malo kumene analembera sakudziwika bwinobwino. Madeti ambiri ndi osatsimikizika. Chizindikiro cha p. chikutanthauza “pambuyo pa,” chizindikiro cha i. chikutanthauza “isanafike” ndipo cha c. chikutanthauza “cha m’ma.”]