Tsamba 2
Kupoletsa Mabala a Kuchitira Nkhanza Ana 3-11
Mamiliyoni a akazi—ndi amuna—akhala minkhole ya kuchitira ana nkhanza yakugonana. M’kope lino, Galamukani! ikulongosola zoyesayesa zamphamvu zimene ambiri akupanga kuti achire ku ziyambukira zake zovulaza.
Kodi Nkuphunziriranji Baibulo? 12
Baibulo ndilo bukhu lakale kwambiri lofalitsidwa koposa onse m’mbiri ya munthu. Kodi nchifukwa ninji muyenera kuliphunzira? Mitani?