Tsamba 2
Kodi Zosangulutsa Zimayambukira Motani Moyo Wanu? 3-10
Kusanguluka ndiko chofunika chabwino cha anthu. Koma moyo wa zosangulutsa ulinso malonda aakulu. Ndipo monga momwedi chikomekome chankhuyu mkati muli nyerere, choteronso sizosangulutsa zonse zimene ziridi zabwino. Kodi ndizosangulutsa zotani zimene mumasankha? Kodi chosankha chanu chimanenanji ponena za inu?
Kupulumutsidwa ku Imfa ndi Chithandizo Chamankhwala Popanda Mwazi 22
Ambiri lerolino amapempha mankhwala opanda mwazi mumkhalidwe wamwadzidzidzi wazamankhwala. Ŵerengani mmene wodwala wina analandirira mankhwala opatsa moyo oterowo.