Tsamba 2
Kodi Pali Chiyembekezo Chotani kwa Ana? 3-11
Tsiku lililonse ana 380,000 amabadwira m’dziko la umphaŵi, njala, matenda, chiwawa, ndi nkhondo. Kodi mwana walero ali ndi chiyembekezo chotani?
Kodi Kuchita Chisoni Nkulakwa? 30
Kodi chiyembekezo chachiukiriro chimachotsapo kufunika kwa kumva chisoni?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Jean-Baptiste Greuze, detail from Le fils puni, Louvre; © Photo R.M.N.