Tsamba 2
Kodi chipembedzo Chikupita? 3-9
Kuwonjezeka kwaposachedwapa kwa chikhulupiriro cha chipembedzo padziko lonse kukupereka chithunzi chonyenga cha zimene zili mtsogolo mwa chipembedzo. Kodi Baibulo limaloseranji?
Kuti Ndilankhule ndi Mwana Wanga, Ndinaphunzira Chinenero China 10
Mayi akusimba za vuto limene anayang’anizana nalo atadziŵa kuti mwana wake anali wogontha.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
CHIKUTO: Manja: Drawings of Albrecht Dürer/Dover Publications, Inc.