Tsamba 2
Kodi Achinyamata Amakono Ali ndi Tsogolo Lotani? 3-10
Kodi nchifukwa chiyani achinyamata ambiri akumamwalira mwamsanga? Ndipo nchifukwa ninji kaŵirikaŵiri amadzipha? Kodi pali njira zothetsera vuto limeneli?
Chinenero Chochita Kuona ndi Maso! 11
Ŵerengani zochitika zodabwitsa ndi zovuta za anthu Ogontha ndi mmene iwo eni amadzimvera. Phunzirani za zilankhulo zawo, mmene amalankhulirana ndi ena.
Kodi Tiyenera Kumuimba Mlandu Satana Chifukwa cha Machimo Athu? 30
Kodi tiyenera kuimba mlandu Satana chifukwa cha machimo athu? Kodi ife eni tili ndi mlandu wotani wa machimo athu?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Erich Lessing/Art Resource, NY