Tsamba 2
Kodi Muyenera Kukambirana za Chipembedzo? 3-9
Kukambirana za chipembedzo mwamtendere kungakhale kovuta. Phunzirani mmene mungakambire mwanjira yomwe ingapindulitsedi.
Kodi Miseche ndi Yoipa Bwanji? 23
Kodi n’chifukwa chiyani anthu ambiri amakonda miseche, koma kuipa kwake n’kotani? Kodi inuyo mungatani?