Tsamba 2
Mmene Mungakhalire ndi Moyo Wautali Komanso Wabwino 3-13
Anthu ambiri akamaganiza za kukalamba amada nkhaŵa, mwina mpaka kuchita mantha. Koma pali zinthu zimene mungathe kuchita zimene zingachititse kuti muthe kukhalabe athanzi pamene mukukalamba.
Mkango Wobangula Usanduka Mwana wa Nkhosa Wofatsa 17
Ŵerengani mumve zimene zinachititsa munthu wina amene anakhala zaka zambiri m’ndende kusinthiratu moyo wake.
N’chifukwa Chiyani Amayi Anga Akudwala Chomwechi? 29
Kuona kholo lanu likudwala ndi kochititsa mantha ndiponso ndi koŵaŵa. Kodi mungatani kuti mupirire?