Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
‘Bwera Ukhale Wotsatira Wanga’
Bukuli sitigulitsa. Timalipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya donate.jw.org.
Malemba onse m’buku lino akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Losindikizidwa mu July 2023
Chichewa (cf-CN)
© 2010, 2023
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA