Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2003
Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo
BAIBULO
Anthu Wamba Anamasulira (Chitahiti), 7/1
Kulunjika Nawo Bwino Mawu a Choonadi, 1/1
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
Chifukwa chake manambala a mavesi m’buku la Masalmo amasiyana, 4/1
Chifuniro cha Mulungu chnachitika kale kumwamba? (Mat. 6:10), 12/15
Ezekieli anakhala wosalankhula? (Ezek. 24:27; 33:22), 12/1
Kubatizidwa chifukwa cha akufa (1 Akor. 15:29, KJ), 10/1
Kulumbira pofuna kunena zoona zokhazokha m’khoti? 1/15
Kumva mawu koma osaona amene akulankhula, ndiye kuti ziwanda n’zimene zikum’vutitsa, 5/1
“Magawo aŵiri” a mzimu wa Eliya (2 Maf. 2:9), 11/1
Mfundo ya mitala inasintha? 8/1
Miyala ya miyezi yobadwira, 11/15
“Mmodzi wa ife” (Gen. 3:22), 10/15
‘Moyo mwa Iye yekha’ (Yoh. 5:26; 6:53), 9/15
Mphatso za ukwati, 9/1
N’chifukwa chiyani munthu ayenera kufuula ngati wina akufuna kumugwirira? 2/1
N’kulakwa kupha galu kapena mphaka? 6/1
“Nthaŵi zonse” (1 Akor. 11:25, 26), 1/1
‘Onani Mlangizi,’ ‘Imvani mawu kumbuyo’ (Yes. 30:20, 21), 2/15
Pamene wodzozedwa yemwe akudwala sangathe kupezekapo pa Chikumbutso, 3/15
Satana ‘ali nayo mphamvu ya imfa’? (Aheb. 2:14), 7/1
Satana amatha kudziŵa zimene munthu akuganiza? 6/15
Ubatizo wa mu 33 C.E. unasonyeza kudzipatulira? 5/15
MBIRI YA MOYO WANGA
Anali Wokoma Mtima (M. Henschel), 8/15
Chimwemwe Chosayerekezeka! (R. Wallwork), 6/1
Kakalata Kamene Kanasintha Moyo Wanga (I. Hochstenbach), 1/1
Kufunafuna Ufumu Choyamba Ndiwo Moyo Wabwino ndi Wosangalatsa (J. Sunal), 3/1
Kuphunzitsidwa ndi Yehova Kuyambira pa Ubwana Wanga (R. Abrahamson), 11/1
Kutumikira Ena Kumachepetsa Mavuto (J. Arias), 7/1
Kuyesedwa mu Ng’anjo Yamoto (P. Yannouris), 2/1
“Ndidzabwezera Yehova Chiyani?” (M. Kerasinis), 12/1
Wodala Munthu Amene Mulungu Wake ndi Yehova (T. Didur), 8/1
Yehova Amakokera Anthu Odzichepetsa (A. Koshino), 10/1
Yehova Amatisamalira Nthaŵi Zonse (E. Mzanga), 9/1
Zimene Ndachitako pa Ntchito ya Padziko Lonse Yophunzitsa Baibulo (R. Nisbet), 4/1
MBONI ZA YEHOVA
Asanaphunzire ndi Ataphunzira, 1/15, 3/15, 5/15, 7/15, 9/15, 11/15
Atumiki a M’mayiko Ena (Dziko la Mexico), 5/1
Chizunzo, 3/1
Dziko la Brazil (gawo la osamva), 2/1
Dziko la Czech Republic, 8/1
Dziko la France, 12/1
Dziko la Poland, 10/1
Dziko la Ukraine, 10/1
Kalendala, 11/15
Khoti Lalikulu Lagamula Kuti Kulambira Koona Kupitirire (Dziko la Armenia), 4/1
Kukumbukira Amene Anaphedwa (Dziko la Hungary), 1/15
Kulalikira Kumakhaladi Kosaiŵalika (Dziko la Mexico), 4/15
Kulambira Koona Kugwirizanitsa Banja, 8/15
Kupindula Chifukwa cha Khama, 1/1
Kuthandizidwa Poonabe Magazi Kukhala Opatulika (Dziko la Philippines), 5/1
‘Linakwaniritsa Chimene Ndinkafuna Kwambiri’ (buku lakuti Yandikirani kwa Yehova), 7/1
Misonkhano ya “Olengeza Ufumu Achangu,” 1/15
Misonkhano ya “Patsani Mulungu Ulemerero,” 3/1
Mmene Anthu Amakhalira pa Msasa wa Anthu Othaŵa Kwawo (Dziko la Tanzania), 2/15
“Moyo Ndi Wokoma!” 1/1
Mwambo Womaliza Maphunziro a Gileadi, 6/15, 12/15
Ogwiritsa Ntchito Chinenero Chapadera (Dziko la Korea), 6/15
“Okonzeka pa Ntchito Iliyonse Yabwino,” 12/1
São Tomé ndi Príncipe, 10/15
Vidiyo Imene Imakhudza Mitima ya Achinyamata, 7/1
MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
Achinyamata, Yendani Moyenera Yehova, 10/15
Achinyamatanu Mukupita Patsogolo Mwauzimu? 4/1
Chikondi, 7/1
Ganizani Bwino Kuti Muchite Zinthu Mwanzeru, 7/15
Khalani ndi Mtima Wopatsa, 11/1
Khalani Okhazikika, 5/15
Kuchita Zinthu Moganizira Ena, 8/1
Kufuna Yehova Mwakhama, 8/15
Kugwiritsira Ntchito Bwino Kusintha kwa Zinthu, 3/1
Kukwanitsidwa ndi Zimene Tili Nazo, 6/1
Kumvetsa Cholinga cha Kulanga, 10/1
Kuona Kuti Okhulupirira Achikulire ndi Ofunika Kwambiri, 9/1
Kupatsa Kumene Kumasangalatsa Mulungu, 6/1
“Limbikani, Ine Ndaligonjetsa Dziko Lapansi,” 3/15
“Malamulo A Wanzeru” (Miy. 13), 9/15
‘Milomo ya Ntheradi’ (Miy. 12), 3/15
‘Mulungu Akomera Mtima Wabwino’ (Miy. 12), 1/15
Mumafunikira Lamulo la M’Baibulo Nthaŵi Zonse? 12/1
“Munalandira Kwaulere, Patsani Kwaulere,” 8/1
‘Musakhale Womangidwa m’Goli ndi Wosiyana,’ 10/15
Musalekerere Mtima wa Mwana Wanu! 2/15
Mwana Wanga Azipita ku Sukulu? 3/15
Tamandani Yehova ‘Pakati pa Msonkhano,’ 9/1
Yehova Amaona Zimene Inu Mumachita? 5/1
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA
Achinyamata Amene Amakondweretsa Mtima wa Yehova, 4/15
Achinyamatanu—Yehova Sadzaiŵala Ntchito Yanu! 4/15
Akazi Achikristu Okhulupirika Ndi Olambira Mulungu Ofunika Kwambiri, 11/1
Akazi Amene Anakondweretsa Mtima wa Yehova, 11/1
Atumiki a Yehova Ali ndi Chiyembekezo Chenicheni (Mika), 8/15
Chitonthozo Chenicheni Chingapezeke Kuti? 5/1
Dalirani Yehova, 9/1
“Dikirani”! 1/1
Imani ndi Kupenya Chipulumutso cha Yehova! 6/1
‘Khalani Amphamvu Ndipo Limbikani Mtima!’ 3/1
Khalani Maso Kuposa Kale Lonse! 1/1
Khalani Okonzekeratu Tsiku la Yehova, 12/15
“Khalani Oyamikira,” 12/1
Khalani Wodziletsa Kuti Mudzalandire Mphoto! 10/15
‘Khalanibe M’mawu Anga,’ 2/1
Khulupirirani Yehova ndi Mtima Wanu Wonse, 3/1
Khulupirirani Yehova Panthaŵi za Mavuto, 9/1
Kodi Chikhulupiriro Chanu N’cholimba Bwanji? 1/15
Kodi Muli ndi Mtima Wodikira? 7/15
Kodi Mumakhulupiriradi Uthenga Wabwino? 1/15
Kodi Yehova Amafuna Chiyani kwa Ife? (Mika), 8/15
‘Kondanani Wina ndi Mnzake,’ 2/1
“Kondwerani mwa Yehova,” 12/1
Kristu Akulankhula ku Mipingo, 5/15
Kufatsa Ndi Khalidwe Lachikristu Lofunika Kwambiri, 4/1
Kukambirana Nkhani Zauzimu Kumalimbikitsa, 9/15
Kupirira Poyesedwa Kumalemekeza Yehova, 10/1
Kutsanzira Mulungu wa Choonadi, 8/1
Kuzunzika Chifukwa cha Chilungamo, 10/1
Lalikirani ndi Cholinga Chopanga Ophunzira, 11/15
‘Lunjikani Nawo Bwino Mawu a Mulungu,’ 11/15
Mgonero wa Ambuye Uli ndi Phindu Lanji kwa Inu? 2/15
Mmene Akristu Oyambirira Anachitira ndi Chilamulo cha Mose, 3/15
“Mubale Chipatso Chambiri,” 2/1
“Mulungu Ndiye Chikondi,” 7/1
Mumafunsa Kuti, “Ali Kuti Yehova?” 5/1
“Musaope, Kapena Kutenga Nkhaŵa,” 6/1
Muziyang’ana Ubwino wa Onse, 6/15
Mverani Zimene Mzimu Ukunena! 5/15
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuchita Chikumbutso cha Mgonero wa Ambuye? 2/15
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera Kosaleka? 9/15
Onani Ena Monga Momwe Yehova Amawaonera, 3/15
Onetsani ‘Kufatsa Konse pa Anthu Onse,’ 4/1
“Taonani, Uyu Ndiye Mulungu Wathu,” 7/1
Thandizani Ena Kulabadira Uthenga wa Ufumu, 11/15
Tidzayenda M’dzina la Yehova Mpaka Muyaya! (Mika), 8/15
Tifunika Kukhala Maso Kwambiri Tsopano, 12/15
Tiziwaona Bwanji Anthu Pamene Tsiku la Yehova Likuyandikira? 7/15
Tonthozani Amene Ali ndi Chisoni, 5/1
Tsanzirani Yehova, Mulungu Wathu Wopanda Tsankho, 6/15
Wonjezerani Kudziletsa pa Chizindikiritso Chanu, 10/15
Yehova, Mulungu wa Choonadi, 8/1
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Alexander VI (papa), 6/15
Anafunafuna Njira Yochepetsetsa (Mgwirizano wa Abale), 12/15
Baibulo Lingathandize Ukwati, 9/15
Baraki, 11/15
Chifukwa chake Mulungu Amalola Mavuto, 1/1
Chikumbutso (Mgonero wa Ambuye), 4/1
Dziko la Paradaiso, 11/15
Eusebius—Kodi Anali “Woyamba Kulemba Mbiri ya Tchalitchi”? 7/15
Guwa la Nsembe N’lofunika Polambira? 2/15
‘Khalani ndi Chikumbumtima Chabwino,’ 5/1
Kodi Mphamvu Zoipa Zapambana? 1/15
Kodi Timafunikadi Anthu Ena? 7/15
Kufukiza, 6/1
Kukoma Mtima Kwachikondi, 4/15
Kuona Mtima, 2/1
Kusangalala Ndiponso Kukhalitsa pa Ntchito, 2/1
Kusankha Zochita, 10/15
Kuthandiza Osoŵa, 6/1
‘Kutsalima Pachothwikira’ (Mac. 26:14), 10/1
Maganizo Abwino pa Nkhani ya Ntchito, 2/1
Martin Luther, 9/15
Mkuyu, 5/15
Moyo Wauzimu, 4/15
‘Mpingo Woona’ Umodzi Wokha? 9/1
Mukufuna Kuti Anthu Adzakukumbukireni Ngati Munthu Wotani? 8/15
N’chiyani Chinaichitikira? (Nofi ndi No), 7/1
Ndani Tingamukhulupirire? 11/1
Nkhani ya Nowa, 5/15
‘Solomo Sanavala Monga Limodzi la Ameneŵa,’ 6/1
Tatian Anali Woikira Kumbuyo Chikristu Kapena Anali Wopanduka? 5/15
Thandizo kwa Anthu Osauka, 9/1
Ugariti—Mzinda Wakale, 7/15
Ukwati wa Boazi ndi Rute, 4/15
Umphaŵi, 3/15, 8/1
Yakobo, 10/15
Zimene Mbalame Zingatiphunzitse, 6/15
Zitsime, 12/1
YEHOVA
Amaganizira Anthu Wamba, 4/15
Amaganiziradi Anthu? 10/1
Amaona Zimene Inu Mumachita? 5/1
Chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhulupirira Mulungu? 12/1
Mafunso Ofunika Kufunsa Mulungu, 5/1
Wofunika Kum’dziŵa, 2/15
YESU KRISTU
Anakhalako Padziko Lapansi? 6/15
Makolo ndi Achibale, 12/15