Zamkatimu
December 15, 2010
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
January 31, 2011–February 6, 2011
Khalani Odzipereka pa Kulambira Koona
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 10, 17
February 7-13, 2011
‘Inoyo Ndiyo Nthawi Yeniyeni Yovomerezeka’
TSAMBA 11
NYIMBO ZOIMBA: 44, 47
February 14-20, 2011
Pezani Madalitso Kudzera mwa Mfumu Yotsogoleredwa ndi Mzimu wa Mulungu
TSAMBA 16
NYIMBO ZOIMBA: 30, 5
February 21-27, 2011
TSAMBA 20
NYIMBO ZOIMBA: 28, 43
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 MASAMBA 7-15
M’nkhani zimenezi tiona mmene Yesu anasonyezera kudzipereka ndiponso zimene tikuphunzira pa chitsanzo chake. Tionanso kuti n’chifukwa chiyani tiyenera kukhala odzipereka kwambiri mu utumiki makamaka masiku ano. Ndiponso tiphunzira kuti n’chifukwa chiyani tinganene kuti inoyo ndiyo nthawi yovomerezeka.
NKHANI YOPHUNZIRA 3 MASAMBA 16-20
Tikukhala m’nthawi imene ulamuliro wa anthu ukulephera. Nkhani iyi itithandiza kuona chifukwa chake Yehova wasankha Yesu Khristu kukhala wolamulira anthu ndiponso madalitso ambirimbiri amene tingapeze ngati tigonjera Khristu.
NKHANI YOPHUNZIRA 4 MASAMBA 20-24
N’chifukwa chiyani tinganene kuti kuimba n’kofunika kwambiri pa kulambira kwathu ndiponso n’kogwirizana ndi Malemba? Nkhani iyi itithandiza kupeza yankho la funso limeneli. Itithandizanso kuona zimene aliyense payekha angachite kuti aziimba.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
Kodi Mwana Wanu Angayankhe Bwanji? 3
Ukalamba Sungatilephe retse Kutumikira Mulungu 25
Ndaona Mphamvu ya Choonadi cha M’Baibulo 26
Mafunso Ochokera kwa Owerenga 30
Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2010 32