Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 10/00 tsamba 2-7
  • Zilengezo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zilengezo
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2000
Utumiki Wathu wa Ufumu—2000
km 10/00 tsamba 2-7

Zilengezo

◼ Mabuku ogaŵira mu October: Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! Paulendo wobwereza mukapeza okondwerera, mungagaŵire masabusikiripishoni. Kuyambira October 16, tidzagaŵira Uthenga wa Ufumu Na. 36. November: Tidzapitiriza kugaŵira Uthenga wa Ufumu Na. 36. Mipingo imene idzamalize kugaŵira eninyumba onse Uthenga wa Ufumu Na. 36 m’gawo lawo ingagaŵire bulosha la Mulungu Amafunanji kapena buku la Chidziŵitso. December: Chidziŵitso Chotsogolera ku Moyo Wosatha. January: Buku lililonse la masamba 192 lofalitsidwa 1986 isanafike limene mpingo ungakhale nalo m’sitoko. Mipingo imene ili ndi buku la Chinsinsi cha Chimwemwe cha Banja ingagaŵirenso buku limeneli.

◼ Mu Utumiki Wathu wa Ufumu uno muli “Ndandanda ya Sukulu ya Utumiki Wateokalase ya 2001” isungeni kuti muigwiritse ntchito chaka chonse cha 2001.

◼ Mapepala oitanira anthu ku Chikumbutso cha 2001 m’chinenero chenicheni cha mpingo uliwonse atumizidwa pamodzi ndi mafomu otumizidwa pachaka.

◼ Mipingo iyenera kuyamba kuoda Kusanthula Malemba Tsiku ndi Tsiku—2001 pamodzi ndi oda yawo yamabuku ya October. Timabukuti tidzakhalako m’Chicheŵa ndi m’Chingelezi. Kufikira pamene timabukuti tidzakhalapo ndi kutumizidwa, tidzaonekera monga “Zoyembekezeredwa” pa mipambo yolongedzera katundu wa mipingo. Timabuku ta Kusanthula Malemba ndi zinthu za oda yapadera.

(Zapitirizidwa pa tsa. 7)

Zilengezo(Zapitirizidwa)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena