Ndandanda ya Mlungu wa September 21
MLUNGU WOYAMBIRA SEPTEMBER 21
Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 26 ndime 8-15
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Numeri 30-32
Na. 1: Numeri 32:1-15
Na. 2: Kodi Chimachitika ndi Chiyani Tikamwalira? (lr-CN mutu 34)
Na. 3: Kodi Akhristu Onse Ali ndi Chiyembekezo Chopita Kumwamba? (rs-CN tsa. 206 ndime 1-3)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Konzekerani Kugawira Nsanja ya Olonda ya October 1 ndi Galamukani! Yapadera ya October. Fotokozani mwachidule zimene zili m’magaziniwa. Pemphani omvera kuti atchule nkhani za m’magazini yapadera ya Galamukani! zimene anthu ambiri a m’gawo lanu angazikonde. Funsani mafunso mpainiya amene ali ndi luso logawira magazini ndipo achite chitsanzo cha mmene angagawirire Galamukani! yapadera.
Mph. 10: Ngati Wina Atanena Kuti, ‘Sindili Wokondwerera.’ Nkhani yokambirana ndi omvera yochokera m’buku la Kukambitsirana tsamba 16. Pemphani wofalitsa kuti achite chitsanzo pogwiritsa mfundo imodzi kapena ziwiri za patsambali.
Mph. 10: “Kugwiritsa Ntchito Baibulo Mwaluso.” Kambiranani mwa mafunso ndi mayankho.