Ndandanda ya Mlungu wa December 7
MLUNGU WOYAMBIRA DECEMBER 7
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 30, ndime 15-23, ndi bokosi patsamba 309
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yoswa 1-5
Na. 1: Yoswa 5:1-15
Na. 2: Mabwenzi Athu Azikhala Okonda Mulungu (lr-CN mutu 44)
Na. 3: Kodi Ufumu wa Mulungu Ndi Chiyani? Zimene Tingachite Posonyeza Kuti Tikuufuna (lr-CN mutu 45)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Kufola Gawo Mwadongosolo. Kambiranani ndi omvera ndime 6, kuyambira pakamutu kakuti “Gawo,” patsamba 102 mpaka tsamba 104, m’buku la Gulu. Funsani woyang’anira utumiki kuti afotokoze dongosolo limene mpingo wanu ukuyendera.
Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Mph. 10: Zindikirani Maganizo a Wofunsayo. Nkhani yokambirana ndi omvera kuchokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, patsamba 66 mpaka tsamba 68.