Ndandanda ya Mlungu wa May 3
MLUNGU WOYAMBIRA MAY 3
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
lv mutu 6 ndime10-15 ndi bokosi la patsamba 67
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: 2 Samueli 1-3
Na. 1: 2 Samueli 2:12-23
Na. 2: Kodi Yesu Ankagwiritsa Ntchito Dzina la Mulungu pa Utumiki Wake?
Na. 3: Kodi Maholide Okumbukira “Mizimu ya Akufa” Anakhazikitsidwa Chifukwa Chiyani? (rs tsa. 244 ndime 1–tsa. 245 ndime 1)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Ngati Mwininyumba wanena kuti, ‘Simumakhulupirira Yesu.’ Nkhani yokambirana ndi omvera kuchokera m’buku la Kukambitsirana, tsamba 433.
Mph. 10: Zosowa za pampingo.
Mph. 10: Sangalalani Pochita Nawo Ulaliki wa Kagulu. Kambiranani ndi omvera kuchokera m’buku la Gulu, patsamba 108 ndime 1-3. Pemphani woyang’anira utumiki kuti anene masiku ndiponso malo okumanira pokonzekera utumiki wakumunda. Pemphani omvera kutchula madalitso amene apeza chifukwa chochita nawo ulaliki umenewu ndiponso chifukwa cholalikira ndi ofalitsa a m’gulu lawo la utumiki wa kumunda.