Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 5/10 tsamba 2
  • Ndandanda ya Mlungu wa May 17

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa May 17
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA MAY 17
Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
km 5/10 tsamba 2

Ndandanda ya Mlungu wa May 17

MLUNGU WOYAMBIRA MAY 17

Nyimbo Na. 49

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

lv mutu 7 ndime 1-9, ndi mabokosi patsamba 76 ndi 78

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: 2 Samueli 9-12

Na. 1: 2 Samueli 10:1-12

Na. 2: N’chifukwa Chiyani Yesu Ankagwiritsa Ntchito Malemba Pophunzitsa? (Yoh. 7:16-18)

Na. 3: Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani Yopanga Zifaniziro Zimene Zimagwiritsidwa Ntchito Polambira? (rs-tsa. 434 ndime 3–tsa. 435 ndime 3)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 12

Mph. 5: Zilengezo.

Mph. 10: Kodi Mungachite Upainiya M’miyezi Ikubwerayi? Nkhani yokambirana ndi omvetsera. Kambiranani mwachidule masamba 112 ndi 113 m’buku la Gulu, pamene afotokoza zofunika kuti munthu ayenerere kukhala mpainiya wothandiza. Pemphani anthu apantchito kapena apasukulu amene anachita upainiya wothandiza ali pa tchuthi kuti afotokoze madalitso amene anapeza.

Mph. 10: Njira Zolalikirira Uthenga Wabwino—Ulaliki Wamwamwayi. Nkhani yokambirana ndi omvetsera yochokera m’buku la Gulu, tsamba 101, ndime 3, mpaka tsamba 102, ndime 2. Ofalitsa afotokoze kapena kuchita chitsanzo chimodzi kapena ziwiri zosonyeza zinthu zosangalatsa zimene zinachitika pochita ulaliki wamwamwayi m’deralo.

Mph. 10: “Atumiki Achikhristu Ayenera Kupemphera.” Nkhani ya mafunso ndi mayankho.

Nyimbo Na. 51

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena