Ndandanda ya Mlungu wa November 21
MLUNGU WOYAMBIRA NOVEMBER 21
Nyimbo Na. 50 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cf mutu 16 ndime 1-6 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Mlaliki 7-12 (Mph. 10)
Na. 1: Mlaliki 9:13–18; 10:1-11 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Chikondi Sichichita Nsanje—1 Akor. 13:4 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Chizindikiro Cha Masiku Otsiriza Chimawakhudza Bwanji Akhristu Oona?—rs tsa. 265 ndime 2 ndi 3 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo. Bokosi la Mafunso. Nkhani.
Mph. 15: Anazunzidwa Chifukwa Chochitira Umboni. (Luka 21:12, 13) Nkhani yokambirana yochokera mu Nsanja ya Olonda ya March 1, 2009, tsamba 12-13, ndime 1 mpaka 10. Komanso kambiranani ndime 2 ndi 3 zokha patsamba 14. Pemphani omvera kuti afotokoze zimene aphunzirapo.
Mph. 10: Magazini Ogawira m’Mwezi wa December. Nkhani yokambirana. Kambiranani nkhani zina za m’magaziniwa ndipo chitani chitsanzo chimodzi kapena ziwiri.
Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero