Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 4/12 tsamba 4
  • Ndandanda ya Mlungu wa May 7

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndandanda ya Mlungu wa May 7
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2012
  • Timitu
  • MLUNGU WOYAMBIRA MAY 7
Utumiki Wathu wa Ufumu—2012
km 4/12 tsamba 4

Ndandanda ya Mlungu wa May 7

MLUNGU WOYAMBIRA MAY 7

Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:

bt mutu 5 ndime 17 mpaka 22 (Mph. 25)

□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:

Kuwerenga Baibulo: Yeremiya 35-38 (Mph. 10)

Na. 1: Yeremiya 36:14-26 (Osapitirira mph. 4)

Na. 2: Kodi Mariya Anakhala Namwali Moyo Wake Wonse?—rs tsa. 255 ndime 5 mpaka tsa. 256 ndime 2 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Zochita Zathu Zingasangalatse Kapena Kukwiyitsa Yehova?—Ower. 2:11-18 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Utumiki:

Nyimbo Na. 91

Mph. 5: Zilengezo.

Mph. 20: Kodi Mwayesapo? Nkhani yokambirana. Fotokozani mfundo za mu nkhani zotsatirazi zimene zinatuluka mu Utumiki Wathu wa Ufumu posachedwapa: “Musalephere Kulalikira” (km 10/11), “Muziponya Nkhonya Zanu Mwanzeru” ndi yakuti, “Muzilalikira Anthu Amene Amalankhula Chinenero China” (km 1/12). Kenako funsani omvera kuti afotokoze mmene agwiritsira ntchito mfundo zopezeka m’nkhanizi ndiponso zimene apindula.

Mph. 10: Zosowa za pampingo.

Nyimbo Na. 14 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena