Ndandanda ya Mlungu wa August 20
MLUNGU WOYAMBIRA AUGUST 20
Nyimbo Na. 44 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 11 ndime 1-4 ndi mabokosi a patsamba 84, 86 ndi 87 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Ezekieli 32-34 (Mph. 10)
Na. 1: Ezekieli 34:15-28 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: Kodi Ndi Malemba Ati Amene Amachititsa Kuti Akhristu Asamachite Nawo Miyambo Yosonyeza Kukonda Dziko Lako?—rs tsa. 372 ndime 3 mpaka tsa. 374 ndime 1 (Mph. 5)
Na. 3: N’chifukwa Chiyani Tinganene Kuti Mapemphero Ochokera Mumtima Amafuna Zambiri?—Sal. 145:18; Mat. 22:37 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Ngati Wina Wanena Kuti: Ndimakhulupirira Kuti Zamoyo Zinachita Kusintha Kuchokera ku Zinthu Zina. Nkhani yokambirana yochokera m’buku la Kukambitsirana patsamba 104, ndime 3 mpaka kumapeto kwa tsamba 106. Chitani chitsanzo chachidule chosonyeza mmene tingayankhire ngati wina atanena kuti, ‘Ndimakhulupirira kuti Mulungu analenga munthu pochita kusandutsa chinthu china chamoyo n’kukhala munthu.’
Mph. 10: Muzilimbikitsana. (Aroma 1:12) Nkhani yokambirana yochokera mu Nsanja ya Olonda ya February 15, 2012, tsamba 20 ndime 8 ndi tsamba 21, ndime 8 ndi 9. Yamikirani mpingo chifukwa cha khama limene umachita mu utumiki.
Mph. 10: “Tetezani Maganizo Anu.” Mafunso ndi mayankho.
Nyimbo Na. 70 ndi Pemphero