Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 May tsamba 6
  • May 23-29

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 23-29
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 May tsamba 6

May 23-29

MASALIMO 19-25

  • Nyimbo Na. 116 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Maulosi Ananena Zokhudza Mesiya”: (10 min.)

    • Sal. 22:1—Mesiya adzaoneka ngati wasiyidwa ndi Mulungu. (w11 8/15 15 ndime 16)

    • Sal. 22:7, 8—Mesiya adzanyozedwa. (w11 8/15 15 ndime 13)

    • Sal. 22:18—Anthu adzachita mayere pa zovala za Mesiya. (w11 8/15 15 ndime 14)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Sal. 19:14—Kodi tingaphunzire chiyani pavesili? (w06 5/15 19 ndime 7)

    • Sal. 23:1, 2—N’chifukwa chiyani tinganene kuti Yehova ndi mbusa wachikondi? (w02 9/15 32 ndime 1-2)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Salimo 25:1-22

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) bh—Werengani lemba pogwiritsa ntchito foni kapena chipangizo china chamakono.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) bh—Gwiritsani ntchito kachizindikiro kofufuzira ka pa JW Library kuti mupeze vesi limene likuyankha funso la mwininyumba.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 129-130 ndime 11-12—Sonyezani mwachidule wophunzirayo mmene angagwiritsire ntchito Laibulale ya JW pokonzekera phunziro la Baibulo pafoni kapena chipangizo china.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 55

  • “Mmene Tingagwiritsire Ntchito Laibulale ya JW”—Gawo 2: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani mavidiyo akuti Pangani Dawunilodi Mabaibulo ndi Fufuzani M’Baibulo Kapena M’Buku, ndipo kambiranani mwachidule zomwe zili m’mavidiyowo. Kenako kambiranani kamutu komaliza m’nkhaniyi. Pemphani abale ndi alongo kuti afotokoze mmene anagwiritsira ntchito Laibulale ya JW mu utumiki.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) cl mutu 30 ndime 19-23, ndi bokosi patsamba 309

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 139 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena