May Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano May 2016 Zitsanzo za Ulaliki May 2-8 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOBU 38-42 Yehova Amasangalala Tikamapempherera Ena MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mumagwiritsa Ntchito Laibulale ya JW? May 9-15 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 1-10 Tizilemekeza Yesu Kuti Tikhale Pamtendere ndi Yehova May 16-22 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 11-18 Ndani Angakhale Mlendo M’chihema cha Yehova? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Mmene Tingagwiritsire Ntchito Laibulale ya JW May 23-29 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 19-25 Zimene Maulosi Ananena Zokhudza Mesiya May 30–June 5 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 26-33 Tizidalira Yehova Kuti Tikhale Olimba Mtima