CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 32-34
Chizindikiro Chosonyeza Kuti Aisiraeli Adzabwerera Kwawo
Losindikizidwa
Yeremiya anatsatira malamulo ofunika pogula munda.
Yehova anasonyeza kuti ndi wabwino polonjeza anthu ake omwe anali ku ukapolo kuti akamvera malangizo ake, adzawakhululukira ndipo adzabwerera ku Isiraeli.