Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 February tsamba 4
  • February 11-17

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 11-17
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 February tsamba 4

February 11-17

AROMA 4-6

  • Nyimbo Na. 20 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mulungu Akuonetsa Chikondi Chake Kwa Ife”: (10 min.)

    • Aroma 5:8, 12​—Yehova anatikonda ngakhale kuti ndife “ochimwa” (w11 6/15 12 ¶5)

    • Aroma 5:13, 14​—Uchimo ndi imfa zakhala zikulamulira ngati mfumu (w11 6/15 12 ¶6)

    • Aroma 5:18, 21​—Yehova anatumiza Mwana wake kuti tidzapeze moyo (w11 6/15 12-13 ¶9-10)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Aroma 6:3-5​—Kodi kubatizidwa “mu mgwirizano ndi Khristu Yesu” komanso “mu imfa yake” kumatanthauza chiyani? (w08 6/15 29 ¶7)

    • Aroma 6:7​—N’chifukwa chiyani anthu amene adzaukitsidwe sadzaweruzidwa chifukwa cha machimo amene anachita asanamwalire? (w14 6/1 11 ¶1)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aroma 4:1-15 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 4)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri. (th phunziro 6)

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako musonyezeni chimodzi mwa zinthu zimene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu. (th phunziro 9)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 107

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 25

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 17 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena