Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsamba 3
  • January 9-15

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 9-15
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 January tsamba 3

January 9-15

2 MAFUMU 24-25

  • Nyimbo Na. 60 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Musamaiwale Kuti Muli mu Nthawi Yamapeto”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mf 24:3, 4​—Kodi mavesiwa akutiphunzitsa chiyani zokhudza Yehova? (w05 8/1 12 ¶1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 24:1-17 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: Pemphero​—1Yo 5:14. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 15)

  • Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza, kenako yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito phunziro 01 la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 19)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 143

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff kubwereza gawo 2

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 54 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena