JUNE 23-29
MIYAMBO 19
Nyimbo Na. 154 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. Muzikhala Bwenzi Lenileni kwa Abale ndi Alongo Anu
(10 min.)
Muzinyalanyaza zolakwa zawo (Miy 19:11; w23.11 12-13 ¶16-17)
Muziwathandiza pamene akufunika thandizo (Miy 19:17; w23.07 9-10 ¶10-11)
Muziwasonyeza chikondi chokhulupirika (Miy 19:22; w21.11 9 ¶6-7)
CHITSANZO: Zimene mumachita ndi abale ndi alongo anu zili ngati zithunzi. Muzisunga zithunzi zabwino zokha zomwe tingaziyerekezere ndi makhalidwe awo abwino.
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Miy 19:1-20 (th phunziro 2)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Popanda kutchula mfundo ya m’Baibulo, pezani njira yomwe ingathandize munthu amene mukukambirana naye kudziwa kuti ndinu wa Mboni za Yehova. (lmd phunziro 2 mfundo 4)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Pa ulendo wapita, munthuyo anakuuzani kuti amasangalala ndi chilengedwe. (lmd phunziro 9 mfundo 4)
6. Nkhani
(5 min.) lmd zakumapeto A mfundo 10—Mutu: Mulungu Ali ndi Dzina. (th phunziro 20)
Nyimbo Na. 40
7. Zofunika Pampingo
(15 min.)
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 28 ¶1-7