OCTOBER 27–NOVEMBER 2
MLALIKI 11-12
Nyimbo Na. 155 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. Muzikhala Athanzi Komanso Osangalala
(10 min.)
Ngati n’zotheka muzipeza nthawi kuti muziwombedwako dzuwa komanso kupitidwako kamphepo (Mla 11:7, 8; g 3/15 13 ¶6-7)
Muzisamalira thanzi lanu komanso muzisamala ndi zimene mumaganiza (Mla 11:10; w23.02 21 ¶6-7)
Koposa zonse, muzilambira Yehova ndi mtima wonse (Mla 12:13; w24.09 2 ¶2-3)
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Mla 12:9, 10—Kodi mavesiwa akutiphunzitsa chiyani zokhudza amuna amene Mulungu anawagwiritsa ntchito kuti alembe Baibulo? (it “Kuuzira” ¶10)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Mla 12:1-14 (th phunziro 12)
4. Ulendo Wobwereza
(3 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. (lmd phunziro 8 mfundo 3)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Pa ulendo wapita, mwininyumbayo anakuuzani kuti wachibale wake kapena mnzake wamwalira. (lmd phunziro 9 mfundo 3)
6. Nkhani
(5 min.) lmd zakumapeto A mfundo 13—Mutu: Mulungu Amafuna Kutithandiza. (th phunziro 20)
Nyimbo Na. 111
7. Zofunika Pampingo
(15 min.)
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) lfb mutu 30-31