DECEMBER 29, 2025–JANUARY 4, 2026
YESAYA 14-16
Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. Adani a Anthu a Mulungu Adzalangidwa
(10 min.)
Babulo wonyada adzawonongedwa kotheratu (Yes 14:13-15, 22, 23; ip-1 180 ¶16; 184 ¶24)
Yehova adzaphwanya Msuri m’dziko lake (Yes 14:24, 25; ip-1 189 ¶1)
Yehova adzachititsa manyazi Mowabu (Yes 16:13, 14; ip-1 194 ¶12)
Left: C. Sappa/DeAgostini via Getty Images; right: Image © Homo Cosmicos/Shutterstock
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Yes 14:1, 2—Kodi zinakhala bwanji kuti anthu a Yehova ‘agwire anthu amene anawagwira n’kupita nawo kudziko lina’? (w06 12/1 10 ¶11)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Yes 16:1-14 (th phunziro 10)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. (lmd phunziro 2 mfundo 5)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KULALIKIRA M’MALO OPEZEKA ANTHU AMBIRI. (lmd phunziro 9 mfundo 4)
6. Nkhani
(5 min.) ijwbq nkhani Na. 108—Mutu: Kodi Ulosi Umatanthauza Chiyani? (th phunziro 14)
Nyimbo Na. 2
7. Zofunika Pampingo
(15 min.)
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) lfb mutu 48-49