Zamkatimu
September 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Mungatani Ngati Mukupanikizika Chifukwa cha Ntchito?
TSAMBA 4 MPAKA 7
12 Zimene Mungachite Kuti Mupewe Matenda a Shuga
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU YA
ACHINYAMATA
Mungapeze mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso ambiri amene mungakhale nawo. Nkhani zake ndi monga:
• “Kodi Ndingafotokoze Bwanji Zimene Ndimakhulupirira pa Nkhani ya Kugonana?”
(Fufuzani pa mawu akuti, ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
Mungathenso kuonera vidiyo yachingelezi yakuti, What Your Peers Say—Procrastination pa webusaiti yathu ya www.jw.org/en.
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandiza ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti, ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > Look under BIBLE TEACHINGS > ANA)