Zamkatimu
Na. 1 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Kodi munthu angamasangalale chifukwa cha mmene amaonera zinthu
Kodi mungayankhe kuti
Inde?
Ayi?
Mwina?
Baibulo limati: “Ukafooka pa tsiku la masautso, mphamvu zako zidzakhala zochepa.”—Miyambo 24:10.
3 NKHANI YA PACHIKUTO
N’zotheka Kumasangalalabe Ngakhale Muli Ndi Mavuto
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
7 Kodi Mumadziwa Zotani Zokhudza a Mboni za Yehova?
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU
NKHANI
Zimene Baibulo limanena zingakudabwitseni.
(Pitani pomwe palembedwa kuti, ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO)
MAVIDIYO
Onerani mavidiyo achingeleziwa kuti mumve zimene achinyamata ena akuchita polimbana ndi mavuto awo.
(Pitani pomwe palembedwa kuti, BIBLE TEACHINGS > TEENAGERS)