Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g19 No. 1 tsamba 16
  • Kodi Munayamba Mwadzifunsapo?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Munayamba Mwadzifunsapo?
  • Galamukani!—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Muzigwiritsa Ntchito Tsamba Loyamba la JW.ORG Mukakhala mu Utumiki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Tingagwiritse Ntchito Bwanji Zinthu Zimene Zinajambulidwa Kuti Tizimvetsera?
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Dziwani Zambiri Zokhudza Zimene Tingachite Kuti Tizikhala Osangalala
    Galamukani!—2018
  • Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?
    Kodi Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo Tingawapeze Kuti?
Onani Zambiri
Galamukani!—2019
g19 No. 1 tsamba 16

KODI MUNAYAMBA MWADZIFUNSAPO?

Bambo ndi mwana wake akuonera limodzi webusaiti ya jw.org
  • Ngati Mulungu amatikondadi, n’chifukwa chiyani amalola kuti tizivutika ndipo n’chifukwa chiyani sakuthetsa mavutowa mpaka pano?

  • Kodi tingatsimikize bwanji kuti tikukhaladi m’masiku otsiriza?

  • Kodi timadziwa bwanji kuti zimene Baibulo linalonjeza zokhudza Ufumu wa Mulungu zidzachitikadi?

  • Kodi mfundo za m’Baibulo zingatithandize tikamasankha zochita panopa?

Mlengi wathu amatikonda kwambiri ndipo watithandiza kupeza mayankho a mafunso amenewa ndi enanso ambiri. Kuti mupeze mayankhowa pitani pawebusaiti yathu ya jw.org. Webusaitiyi inakonzedwa ndi cholinga chothandiza anthu kuphunzira Baibulo.

Pawebusaitiyi mungathe kupezaponso mavidiyo, zinthu zongomvetsera, zochitika pa moyo wa anthu ena, mabuku osiyanasiyana komanso Baibulo. Mungathe kupanga dawunilodi zinthu zonsezi kwaulere.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena