Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ssb nyimbo 212
  • Tikuyamikani, Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tikuyamikani, Yehova
  • Imbirani Yehova Zitamando
  • Nkhani Yofanana
  • Tikuyamikani Yehova
    Imbirani Yehova
  • Tikukuthokozani Yehova
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Pemphero la Mtumiki wa Mulungu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Kodi Umakumbukira Kunena Kuti Zikomo?
    Phunzirani kwa Mphunzitsi Waluso
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Zitamando
Ssb nyimbo 212

Nyimbo 212

Tikuyamikani, Yehova

(1 Atesalonika 5:18)

1. Tiyamika Ya, usana usiku,

Munatipatsa kuŵala kwanu.

Tiyamika chifukwa cha pemphero,

Kuti tikhoze kukufikani.

2. Tiyamika Ya, ka’mba ka Mwana’nu,

Anapambana imfa mumanda.

Tiyamika ka’mba ka chitsogozo,

Kukwaniritsa zowinda zathu.

3. Tiyamika Ya, ka’mba ka ubale,

Tipeza mabwenzi owonadi.

Tiyamika ka’mba ka mzimu wanu,

Umene umatithandizadi.

4. Tiyamika Ya, chifukwa cha ntchito

Yakulali ka za dzina lanu.

Tiyamika mudzachotsa matsoka,

Madalitso anu ndi osatha.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena