Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • jy tsamba 320
  • Maulosi Ena Onena za Mesiya

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Maulosi Ena Onena za Mesiya
  • Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Maulosi Onena za Mesiya Amatsimikizira Kuti Yesu Analidi Mesiya?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • Yesu Ndi Mesiya Amene Mulungu Ananeneratu Kuti Adzabwera
    Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?
  • Kupanga Dziko Limodzi Pansi pa Ufumu wa Mulungu
    Mbiri Yabwino Yokusangalatsani
  • Mesiya
    Galamukani!—2015
Onani Zambiri
Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo
jy tsamba 320

Maulosi Ena Onena za Mesiya

ZIMENE ZINACHITIKA

ULOSI

KUKWANIRITSIDWA KWAKE

MUTU

Anabadwira ku Betelehemu

Mika 5:2

Luka 2:1-6

5, 7, 67

Anathawa kenako n’kubwereranso ku Iguputo

Hoseya 11:1

Mateyu 2:13-15, 19, 20

8

Azimayi analirira ana awo ataphedwa pofuna kupha Yesu ali mwana

Yeremiya 31:15

Mateyu 2:17, 18

8

Analengeza za ufulu kwa anthu ogwidwa

Yesaya 61:1, 2

Luka 4:17-21

21

Anakhala ku Kaperenao m’chigawo cha Galileya

Yesaya 9:1, 2

Mateyu 4:13-17

22, 67

Anachiritsa anthu ambiri odwala

Yesaya 53:4

Mateyu 8:16, 17

23

Sanafuule m’misewu

Yesaya 42:1-4

Mateyu 12:16-21

33

Ankagwiritsa ntchito mafanizo pophunzitsa

Salimo 78:2; Yesaya 6:9, 10

Mateyu 13:13-15, 34, 35

43

Analowa mu Yerusalemu atakwera pabulu

Zekariya 9:9

Mateyu 21:1-9

102

Anthu ambiri sanamukhulupirire

Yesaya 6:10; 53:1

Yohane 12:37, 38

104

Mnzake amene ankamukhulupirira anamupereka

Salimo 41:9

Yohane 13:18, 21

117

Ophunzira ake anathawa n’kumusiya yekha

Zekariya 13:7

Mateyu 26:31, 54-56

118, 124

Anthu anadana naye popanda chifukwa

Salimo 35:19; 69:4

Yohane 15:24, 25

120

Asilikali anagawana zovala zake

Salimo 22:18

Yohane 19:23, 24

131

Anamva ludzu ali pamtengo

Salimo 22:15

Yohane 19:28

132

Anamubaya atafa kale

Zekariya 12:10

Yohane 19:34, 37

133

Mafupa ake sanathyoledwe ngakhale asanamwalire

Salimo 34:20

Yohane 19:36

133

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena