Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • CO-pgm17 tsamba 2-3
  • Lachisanu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Lachisanu
  • Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2017
  • Nkhani Yofanana
  • Lachisanu
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2019
  • Lamlungu
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2024
  • Loweruka
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2017
  • Lachisanu
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2024
Onani Zambiri
Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2017
CO-pgm17 tsamba 2-3

Lachisanu

“Tisaleke kuchita zabwino”​—AGALATIYA 6:9

M’MAWA

  • 9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo

  • 9:30 Nyimbo Na. 143 ndi Pemphero

  • 9:40 NKHANI YA TCHEYAMANI: Tisafooke, Makamaka Panopa (Chivumbulutso 12:12)

  • 10:15 NKHANI YOSIYIRANA: Pitirizani Kulalikira “Mwakhama”

    • Mwamwayi (Machitidwe 5:42; Mlaliki 11:6)

    • Kunyumba ndi Nyumba (Machitidwe 20:20)

    • M’malo Opezeka Anthu Ambiri (Machitidwe 17:17)

    • Muzithandiza Anthu Kuti Akhale Ophunzira a Yesu (Aroma 1:14-16; 1 Akorinto 3:6)

  • 11:05 Nyimbo Na. 153 ndi Zilengezo

  • 11:15 SEWERO LA MAWU OKHA: Yehova Amapulumutsa Anthu Ake (Ekisodo 3:1-22; 4:1-9; 5:1-9; 6:1-8; 7:1-7; 14:5-10, 13-31; 15:1-21)

  • 11:45 Yehova Ndi Chitsanzo Chabwino Kwambiri pa Nkhani ya Kupirira (Aroma 9:22, 23; 15:13; Yakobo 1:2-4)

  • 12:15 Nyimbo Na. 35 ndi Kupuma

MASANA

  • 1:25 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo

  • 1:35 Nyimbo Na. 135

  • 1:40 NKHANI YOSIYIRANA: Tizikhalabe Okhulupirika . . .

    • Ena Akamatichitira Zopanda Chilungamo (Mateyu 5:38, 39)

    • Ngati Tikuvutika Chifukwa cha Ukalamba (Yesaya 46:4; Yuda 20, 21)

    • Ngakhale Kuti Si Ife Angwiro (Aroma 7:21-25)

    • Tikapatsidwa Chilango pa Zimene Tinalakwitsa (Agalatiya 2:11-14; Aheberi 12:5, 6, 10, 11)

    • Ngati Tikudwala Matenda Okhalitsa (Salimo 41:3)

    • Tikaferedwa (Salimo 34:18)

    • Tikamazunzidwa (Chivumbulutso 1:9)

  • 2:55 Nyimbo Na. 85 ndi Zilengezo

  • 3:05 SEWERO: Kumbukirani Mkazi wa Loti​—Mbali Yoyamba (Luka 17:28-33)

  • 3:35 NKHANI YOSIYIRANA: Zimene Zingatithandize Kuti Tizitha Kupirira

    • Chikhulupiriro (Aheberi 11:1)

    • Makhalidwe Abwino (Afilipi 4:8, 9)

    • Kudziwa Zinthu (Miyambo 2:10, 11)

    • Kudziletsa (Agalatiya 5:22, 23)

  • 4:15 Tingatani Kuti ‘Tisalephere Ngakhale Pang’ono’? (2 Petulo 1:5-10; Yesaya 40:31; 2 Akorinto 4:7-9, 16)

  • 4:50 Nyimbo Na. 152 ndi Pemphero Lomaliza

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena