Lamlungu
“. . . kenako mapeto adzafika”—Mateyu 24:14
M’mawa
8:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 84 Komanso Pemphero
8:40 NKHANI YOSIYIRANA: Muzitsanzira Anthu Amene Ankakhulupirira Uthenga Wabwino
• Zekariya (Aheberi 12:5, 6)
• Elizabeti (1 Atesalonika 5:11)
• Mariya (Salimo 77:12)
• Yosefe (Miyambo 1:5)
• Simiyoni ndi Ana (1 Mbiri 16:34)
• Yesu (Yohane 8:31, 32)
10:05 Nyimbo Na. 65 Komanso Zilengezo
10:15 NKHANI YA ONSE: N’chifukwa Chiyani Sitimaopa Uthenga Woipa? (Salimo 112:1-10)
10:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
11:15 Nyimbo Na. 61 Komanso Kupuma
Masana
12:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 122
12:50 KUWERENGA BAIBULO MWASEWERO: “Nthawi Yodikira Yatha” (Chivumbulutso 10:6)
1:20 Nyimbo Na. 126 Komanso Zilengezo
1:30 Kodi Mwaphunzira Chiyani?
1:40 N’chifukwa Chiyani Tikufunika ‘Kugwira Mwamphamvu Uthenga Wabwino’ Nanga Tingachite Bwanji Zimenezi? (1 Akorinto 2:16; 15:1, 2, 58; Maliko 6:30-34)
2:30 Nyimbo Yatsopano Komanso Pemphero Lomaliza