Lamlungu
“Amene adzapirire mpaka pa mapeto, ndiye amene adzapulumuke”—MATEYU 24:13
M’MAWA
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 83 ndi Pemphero
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Tiyenera ‘Kuthamanga Mopirira’
Tizithamanga M’njira Yoti Tikalandire Mphoto (1 Akorinto 9:24)
Muziphunzira Mwakhama (1 Akorinto 9:25-27)
Tizipewa Zinthu Zosafunika Zomwe Zingangotitopetsa (Aheberi 12:1)
Muzitsanzira Anthu Achitsanzo Chabwino (Aheberi 12:2, 3)
Muzidya Chakudya Chopatsa Thanzi (Aheberi 5:12-14)
Muzimwa Madzi Ambiri (Chivumbulutso 22:17)
Muzitsatira Malamulo a Mpikisano (2 Timoteyo 2:5)
Musamakayikire Kuti Mudzapeza Mphoto (Aroma 15:13)
11:10 Nyimbo Na. 130 ndi Zilengezo
11:20 NKHANI YA ONSE: Musataye Mtima! (Yesaya 48:17; Yeremiya 29:11)
11:50 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
12:20 Nyimbo Na. 148 ndi Kupuma
MASANA
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:45 Nyimbo Na. 142
1:50 SEWERO: Kumbukirani Mkazi wa Loti—Mbali Yachitatu (Luka 17:28-33)
2:20 Nyimbo Na. 65 ndi Zilengezo
2:30 “Uziwayembekezerabe . . . Iwo Sadzachedwa” (Habakuku 2:3)
3:30 Nyimbo Na. 154 ndi Pemphero Lomaliza