Lamlungu
“Adzalambira Atate motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi”—Yohane 4:23
M’mawa
8:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 140 Komanso Pemphero
8:40 NKHANI YOSIYIRANA: Zimene Tikuphunzira pa Zomwe Yesu Ananena
• “Kubadwa mwa Madzi ndi Mzimu” (Yohane 3:3, 5)
• “Palibe Munthu Amene Anakwera Kumwamba” (Yohane 3:13)
• ‘Fikani Pamene Pali Kuwala’ (Yohane 3:19-21)
• “Munthu Ameneyo Ndi Ineyo” (Yohane 4:25, 26)
• “Chakudya Changa” (Yohane 4:34)
• “M’mindamo . . . Mwayera Kale Ndipo M’mofunika Kukolola” (Yohane 4:35)
10:05 Nyimbo Na. 37 Komanso Zilengezo
10:15 NKHANI YA ONSE: Kodi Zomwe Mumakhulupirira Ndi Zoona? (Yohane 4:20-24)
10:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
11:15 Nyimbo Na. 84 Komanso Kupuma
Masana
12:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 77
12:50 VIDIYO:
Uthenga Wabwino wa Yesu: Gawo 3
“Munthu Ameneyo Ndi Ineyo” (Yohane 3:1–4:54; Mateyu 4:12-20; Maliko 1:19, 20; Luka 4:16–5:11)
1:35 Nyimbo Na. 20 Komanso Zilengezo
1:45 Kodi Mwaphunzira Chiyani?
1:55 Pitirizani Kukhala M’kachisi Wamkulu Wauzimu wa Yehova (Aheberi 10:21-25; 13:15, 16; 1 Petulo 1:14-16; 2:21)
2:45 Nyimbo Yatsopano Komanso Pemphero Lomaliza