Loweruka
“Khalani oleza mtima kwa onse” 1 Atesalonika 5:14
M’Mawa
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 58 ndi Pemphero
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: ‘Timasonyeza Kuti Ndife Atumiki a Mulungu . . . mwa Kukhala Oleza Mtima’
• Tikamalalikira (Machitidwe 26:29; 2 Akorinto 6:4, 6)
• Tikamaphunzira Baibulo ndi Anthu (Yohane 16:12)
• Tikamalimbikitsana (1 Atesalonika 5:11)
• Tikamatumikira Monga Mkulu (2 Timoteyo 4:2)
10:30 Muzileza Mtima Chifukwa Inunso Munasonyezedwa Kuleza Mtima (Mateyu 7:1, 2; 18:23-35)
10:50 Nyimbo Na. 138 ndi Zilengezo
11:00 NKHANI YOSIYIRANA: ‘Moleza Mtima, Muzilolerana M’chikondi’
• Achibale Omwe Si a Mboni (Akolose 4:6)
• Mwamuna Kapena Mkazi Wanu (Miyambo 19:11)
• Ana Anu (2 Timoteyo 3:14)
• Achibale Amene Akudwala Kapena Omwe Ndi Achikulire (Aheberi 13:16)
11:45 NKHANI YA UBATIZO: Kuleza Mtima kwa Yehova Kumatithandiza Kuti Tidzapulumuke (2 Petulo 3:13-15)
12:15 Nyimbo Na. 75 ndi Kupuma
Masana
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:45 Nyimbo Na. 106
1:50 N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupewa Kusangalala ndi Zinthu Zosakhalitsa? (1 Atesalonika 4:3-5; 1 Yohane 2:17)
2:15 NKHANI YOSIYIRANA: “Munthu Woleza Mtima Ndi Wabwino Kuposa Munthu Wodzikuza”
• Muzitsanzira Abele, Osati Adamu (Mlaliki 7:8)
• Muzitsanzira Yakobo, Osati Esau (Aheberi 12:16)
• Muzitsanzira Mose, Osati Kora (Numeri 16:9, 10)
• Muzitsanzira Samueli, Osati Sauli (1 Samueli 15:22)
• Muzitsanzira Yonatani, Osati Abisalomu (1 Samueli 23:16-18)
3:15 Nyimbo Na. 87 ndi Zilengezo
3:25 VIDIYO: ‘Muzilola Kuti Yehova Akutsogolereni’—Mbali Yoyamba (Salimo 37:5)
3:55 “Pozunzidwa, Timapirira” Moleza Mtima (1 Akorinto 4:12; Aroma 12:14, 21)
4:30 Nyimbo Na. 79 ndi Pemphero Lomaliza