Lamlungu
‘Yehova akuyembekezera moleza mtima kuti akukomereni mtima’ Yesaya 30:18
M’mawa
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 95 ndi Pemphero
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Tengerani Chitsanzo cha Kuleza Mtima kwa Aneneri
• Eliya (Yakobo 5:10, 17, 18)
• Mika (Mika 7:7)
• Hoseya (Hoseya 3:1)
• Yesaya (Yesaya 7:3)
• Ezekieli (Ezekieli 2:3-5)
• Yeremiya (Yeremiya 15:16)
• Danieli (Danieli 9:22, 23)
11:05 Nyimbo Na. 142 ndi Zilengezo
11:15 NKHANI YA ONSE: Kodi Mulungu Angakuthandizenidi? (Yesaya 64:4)
11:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
12:15 Nyimbo Na. 94 ndi Kupuma
Masana
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:45 Nyimbo Na. 114
1:50 VIDIYO: ‘Muzilola Kuti Yehova Akutsogolereni’—Mbali Yachiwiri (Salimo 37:5)
2:30 Nyimbo Na. 115 ndi Zilengezo
2:40 ‘Yehova Akuyembekezera Moleza Mtima Kuti Akukomereni Mtima’ (Yesaya 30:18-21; 60:17; 2 Mafumu 6:15-17; Aefeso 1:9, 10)
3:40 Nyimbo Yatsopano Komanso Pemphero Lomaliza