Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 7/96 tsamba 7
  • ‘Pitirizani Kukula m’Chidziŵitso Cholongosoka’

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • ‘Pitirizani Kukula m’Chidziŵitso Cholongosoka’
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—1996
  • Nkhani Yofanana
  • Chifukwa Chimene Timafunikira Chidziŵitso Cholongosoka
    Nsanja ya Olonda—1989
  • Thandizani Ena Kupeza Chidziŵitso Chotsogolera ku Moyo
    Utumiki Wathu wa Ufumu—1996
  • Kodi Mumafunafuna Chuma Chobisika?
    Nsanja ya Olonda—1989
  • “Moyo Wosatha ndi Uwu”
    Utumiki Wathu wa Ufumu—1996
Onani Zambiri
Utumiki Wathu wa Ufumu—1996
km 7/96 tsamba 7

‘Pitirizani Kukula m’Chidziŵitso Cholongosoka’

Chidziŵitso cholongosoka cha Mulungu chimatsogolera ku moyo wosatha. (Yoh. 17:3) Tiyenera kumachita zonse zimene tingathe kuti tiwonjezere chidziŵitso cholongosoka chonena za Yehova. (Akol. 1:9, 10) Kuyamba pa August 5, tidzaphunzira buku la Chidziŵitso Chotsogolera ku Moyo Wosatha pa Phunziro la Buku la Mpingo. Si kuzindikira kwathu Mawu a Mulungu kokha kumene kudzakuzidwa komanso tidzakhala okonzekeretsedwa bwino kwambiri kuwaphunzitsa kwa ena. Inu ndi banja lanu mudzadalitsidwa ngati mukonzekera pasadakhale, kufika ndi kutengamo mbali mlungu uliwonse, ndi kugwiritsira ntchito chidziŵitso chimenecho mu utumiki.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena