Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 June tsamba 5
  • Ezekieli Anasangalala Kulengeza Uthenga wa Mulungu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ezekieli Anasangalala Kulengeza Uthenga wa Mulungu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Mmene Yehova Amatithandizira Kukwaniritsa Utumiki Wathu
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2022
  • Mfundo Zazikulu za M’buku la Ezekieli—Gawo 1
    Nsanja ya Olonda—2007
  • Mvetserani—Mlonda wa Yehova Akulankhula!
    Nsanja ya Olonda—1988
  • “Iri Ndi Tsiku la Masiku Onse”
    Nsanja ya Olonda—1988
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 June tsamba 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 1-5

Ezekieli Ankasangalala Kulengeza Uthenga wa Mulungu

M’masomphenya, Yehova anapatsa Ezekieli mpukutu n’kumuuza kuti adye. Kodi zimenezi zinkatanthauza chiyani?

2:9–3:2

  • Ezekieli ankafunika kuwerenga komanso kumvetsa bwino uthenga wa Mulungu. Kusinkhasinkha zimene ankawerenga mumpukutu kunachititsa kuti uthenga wake umufike pamtima ndipo izi zinamulimbikitsa kuti aziuza ena

3:3

  • Ezekieli ankamva kuti mpukutuwo unkatsekemera chifukwa choti anasangalala ndi ntchito imene anapatsidwa

Ezekieli anapita kukalankhula ndi anthu a ku Isiraeli pambuyo podya mpukutu womwe unkaimira uthenga wa Mulungu

Kodi kuphunzira Baibulo ndi kusinkhasinkha kungandithandize bwanji?

Kodi ndingatani kuti ndizisangalala ndi ntchito yolalikira?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena