Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 June tsamba 2
  • Muzitsatira Mapazi a Khristu Mosamala Kwambiri

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzitsatira Mapazi a Khristu Mosamala Kwambiri
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • ONERANI VIDIYO YAKUTI DZINA LA YEHOVA NDI LOFUNIKA KWAMBIRI, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:
  • Muzisangalala Mukamazunzidwa
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • “Ganizirani Mozama za Munthu Amene Anapirira”
    ‘Bwera Ukhale Wotsatira Wanga’
  • Kupirira Mavuto Kuli Ndi Ubwino Wake
    Nsanja ya Olonda—2007
  • N’zotheka Kupirira Ena Akamakuzunzani
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 June tsamba 2

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzitsatira Mapazi a Khristu Mosamala Kwambiri

Yesu anatipatsa chitsanzo choti tizitsatira makamaka tikamakumana ndi mayesero kapena tikamazunzidwa. (1 Pet. 2:21-23) Iye sanabwezere anthu amene ankamunyoza ndipo sanachite zimenezi ngakhale pa nthawi imene ankamva ululu. (Maliko 15:29-32) Kodi n’chiyani chinamuthandiza kuti apirire? Iye anali wofunitsitsa kuchita chifuniro cha Yehova. (Yoh. 6:38) Yesu ankaganiziranso kwambiri za “chimwemwe chimene anamuikira patsogolo pake.”​—Aheb. 12:2.

Kodi ifeyo timatani ngati anthu ena akutizunza chifukwa cha zimene timakhulupirira? Akhristu oona ‘sabwezera choipa pa choipa.’ (Aroma 12:14, 17) Tikamatsanzira Yesu n’kumapirira, tingakhalebe osangalala podziwa kuti Yehova akukondwera nafe.​—Mat. 5:10-12; 1 Pet. 4:12-14.

ONERANI VIDIYO YAKUTI DZINA LA YEHOVA NDI LOFUNIKA KWAMBIRI, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi Mlongo Pötzingera anagwiritsa ntchito bwanji nthawi yake mwanzeru pamene anamutsekera m’selo yayekha?

  • Kodi M’bale ndi Mlongo Pötzinger anakumana ndi mavuto otani pamene anali m’ndende zosiyanasiyana?

  • Kodi n’chiyani chinawathandiza kuti apirire?

Azimayi akugwira ntchito yakalavulagaga kundende ya Nazi; M’bale ndi Mlongo Pöetzinger

Muzitsatira mapazi a Khristu mosamala kwambiri mukamazunzidwa

a Dzinali limalembedwanso kuti Poetzinger.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena