Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 September tsamba 5
  • Chilango Chimasonyeza Kuti Yehova Amatikonda

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Chilango Chimasonyeza Kuti Yehova Amatikonda
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Kupatsidwa Chilango Kumasonyeza Kuti Yehova Amatikonda
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Kumvetsa Cholinga cha Kulanga
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Timasonyeza Chikondi Tikamachita Zinthu Mogwirizana Ndi Chilango Chochokera kwa Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Mulungu Amatilangiza Chifukwa Chotikonda
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 September tsamba 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 12-13

Chilango Chimasonyeza Kuti Yehova Amatikonda

12:5-7, 11

Mayi akuwerengera mwana wake wamkazi buku la “Phunzirani kwa Mphunzitsi Waluso.”

M’Baibulo mawu akuti chilango angatanthauze kudzudzula, kulangiza komanso kuphunzitsa. Monga mmene bambo wachikondi amachitira, nayenso Yehova amatipatsa chilango. Amatilangiza kapena kutipatsa chilangochi:

  • Tikamawerenga Baibulo, kuphunzira patokha, tikakhala pamisonkhano komanso tikamasinkhasinkha

  • Tikamalandira uphungu kapena malangizo kuchokera kwa Akhristu anzathu

  • Polola kuti tikumane ndi zotsatirapo za zimene talakwitsa

  • Tikadzudzulidwa kapena kuchotsedwa mumpingo

  • Polola kuti tikumane ndi mayesero kapena chizunzo.​—w15 9/15 21 ¶13; it-1 629

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena