CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 46-47
Chakudya pa Nthawi ya Njala
Masiku ano anthu ambiri akuvutika ndi njala yauzimu. (Amosi 8:11) Pogwiritsa ntchito Yesu Khristu, Yehova amatipatsa chakudya chambiri chauzimu chimene chimatithandiza.
Mabuku athu
Misonkhano ya mpingo
Misonkhano yadera ndi yachigawo
Zinthu zongomvetsera
Mavidiyo
JW.ORG
JW Broadcasting
Kodi ndikudzimana zinthu ziti kuti ndizidya patebulo la Yehova nthawi zonse?