Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 August tsamba 6
  • Amuna Odzichepetsa Amaphunzitsa Ena N’kumawapatsa Zochita

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Amuna Odzichepetsa Amaphunzitsa Ena N’kumawapatsa Zochita
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Akulu—Gaŵirani Mathayo!
    Nsanja ya Olonda—1992
  • ‘Zinthu Zimenezo Uziziphunzitsa kwa Anthu Okhulupirika’
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • Muzipatsa Ena Ntchito Zina
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Kudzichepetsa N’kofunika Kwambiri
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 August tsamba 6
Zithunzi: Mkulu wodziwa zambiri akuphunzitsa m’bale pang’onopang’ono n’cholinga choti azichita zambiri mumpingo. 1. M’bale uja wagwira maikofoni pamene mkulu wodziwa zambiri akupereka ndemanga pamisonkhano. 2. M’bale uja wapita limodzi ndi mkulu wodziwa zambiri uja ku maulendo a ubusa. 3. M’bale uja tsopano wakhala mkulu ndipo akulankhula pamsonkhano wa akulu. 4. Mkulu watsopano uja akuchititsa Phunziro la Nsanja ya Olonda. Mkulu wodziwa zambiri uja ndi amene akuwerenga.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 17-18

Amuna Odzichepetsa Amaphunzitsa Ena N’kumawapatsa Zochita

18:17, 18, 21, 22, 24, 25

Abale odziwa zambiri amachita bwino akamaphunzitsa achinyamata kenako n’kuwapatsa zochita. Akamachita zimenezi amasonyeza kudzichepetsa, chikondi komanso kuti amaona zakutsogolo. Angachite bwanji zimenezi?

  • Sankhani abale amene akuoneka kuti akhoza kukwanitsa kusamalira maudindo ena

  • Afotokozereni momveka bwino zimene ayenera kuchita pogwira ntchitoyo

  • Ngati pangafunike ndalama, zipangizo, kapena zinthu zina kuti agwire bwino ntchitoyo, muziwapatsa zimenezo

  • Muziona mmene akugwirira ntchitoyo ndipo muziwasonyeza kuti mukuwadalira

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndi zochita ziti zimene ndingapereke kwa ena?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena