Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 December tsamba 4
  • Zimene Tingaphunzire pa Malamulo Okhudza Khate

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Tingaphunzire pa Malamulo Okhudza Khate
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Moyo Wanga Monga Wakhate—Wachimwemwe ndi Wodalitsidwa Mwauzimu Yosimbidwa ndi Isaiah Adagbona
    Nsanja ya Olonda—1998
  • Kodi Mukudziwa?
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda—2009
  • “Ngwazi ya Nkhokera”
    Galamukani!—1987
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 December tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 12-13

Zimene Tingaphunzire pa Malamulo Okhudza Khate

13:4, 5, 45, 46, 52, 57

Kodi mfundo za m’malamulo okhudza khate zingatiphunzitse chiyani pa nkhani ya kuteteza moyo wathu wauzimu?

  • Yehova anaphunzitsa ansembe zimene angachite kuti azindikire khate likangoyamba. Masiku anonso, abusa a Chikhristu amathandiza mwachangu munthu amene wayamba kudwala mwauzimu.​—Yak 5:14, 15

  • Aisiraeli ankafunika kuwononga chinthu chilichonse chodetsedwa ndi khate kuti matendawo asafalikire. Akhristu nawonso ayenera kusiya chilichonse, ngakhale chimene amachikonda kwambiri, chomwe chingawachititse kuchimwa. (Mt 18:8, 9) Zimenezi zingaphatikizepo zinthu monga makhalidwe awo, anzawo komanso zosangalatsa

Mzimayi akukanitsitsa kuyambiranso moyo wake wakale womwa mowa kwambiri.

Kodi Mkhristu angasonyeze bwanji kuti akufuna kuthandizidwa ndi Yehova?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena