Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsamba 4
  • ‘Mukathamangitse Anthu Onse a M’dzikolo’

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • ‘Mukathamangitse Anthu Onse a M’dzikolo’
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Amatsogolera Anthu Ake
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Mmene Chikhulupiriro Chimatithandizira Kukhala Olimba Mtima
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Samalani ndi Nkhani Zabodza
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Zimene Tingaphunzire pa Zomwe Zinkachitika pa Msasa wa Aisiraeli
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 May tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

‘Mukathamangitse Anthu Onse a M’dzikolo’

Yehova analamula anthu ake akuti akachotse chilichonse chimene chikanawachititsa kuti asakhale okhulupirika m’Dziko Lolonjezedwa (Nu 33:52; w10 8/1 23)

Yehova anawauza kuti adzawathandiza kuti alande dzikolo (Nu 33:53)

Aisiraeli akanadzibweretsera mavuto ambiri akanasiya adani awo ena osawagonjetsa (Nu 33:55, 56; w08 2/15 27 ¶5-6; it-1 404 ¶2)

Kuti tizisangalatsa Yehova, tiyenera kusiya chilichonse chimene chingawononge makhalidwe athu abwino komanso kutisokoneza mwauzimu. (Yak 1:21) Yehova amatipatsa mphamvu kuti tithe kulimbana ndi makhalidwe athu oipa komanso kuti tisatengere zinthu zoipa za m’dzikoli.

Anyamata atatu akusewera gemu yachiwawa mosangalala.
Wachinyamata akuthimitsa TV.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena